Hagai 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ‘Ulemerero wa nyumba yatsopanoyi udzakhala waukulu kuposa wa nyumba yoyamba ija,’+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. ‘Ndipo ndidzakupatsani mtendere pamalo ano,’+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.” Hagai Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:9 Nsanja ya Olonda,12/1/2007, tsa. 91/1/1997, ptsa. 9, 227/1/1996, ptsa. 12-13, 18-196/1/1989, tsa. 30
9 ‘Ulemerero wa nyumba yatsopanoyi udzakhala waukulu kuposa wa nyumba yoyamba ija,’+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. ‘Ndipo ndidzakupatsani mtendere pamalo ano,’+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.”
2:9 Nsanja ya Olonda,12/1/2007, tsa. 91/1/1997, ptsa. 9, 227/1/1996, ptsa. 12-13, 18-196/1/1989, tsa. 30