Mateyu 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Choncho gulu la anthulo linadabwa kuona anthu osalankhula akulankhula, olumala akuyenda ndiponso anthu osaona akuona ndipo anatamanda Mulungu wa Isiraeli.+
31 Choncho gulu la anthulo linadabwa kuona anthu osalankhula akulankhula, olumala akuyenda ndiponso anthu osaona akuona ndipo anatamanda Mulungu wa Isiraeli.+