-
Mateyu 22:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Kenako inatumanso akapolo ena kuti, ‘Kauzeni oitanidwawo kuti: “Ine ndakonza chakudya chamasana, ngʼombe zanga zamphongo komanso nyama zanga zonenepa zaphedwa, ndipo zinthu zonse zakonzedwa kale. Bwerani kuphwando laukwati.”’
-