Mateyu 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako inatumanso akapolo ena+ kuti, ‘Kauzeni oitanidwawo kuti: “Ine ndakonza chakudya chamasana,+ ng’ombe zanga komanso nyama zanga zonenepa zaphedwa, ndipo zinthu zonse zakonzedwa kale. Bwerani ku phwando laukwati.”’+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:4 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 248-249 Nsanja ya Olonda,1/15/2008, tsa. 311/15/1990, tsa. 8
4 Kenako inatumanso akapolo ena+ kuti, ‘Kauzeni oitanidwawo kuti: “Ine ndakonza chakudya chamasana,+ ng’ombe zanga komanso nyama zanga zonenepa zaphedwa, ndipo zinthu zonse zakonzedwa kale. Bwerani ku phwando laukwati.”’+