Maliko 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atatero, anaitana gulu la anthuwo kuti abwerenso kwa iye ndipo anawauza kuti: “Mvetserani kuno nonsenu, ndipo mumvetse tanthauzo lake.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:14 Nsanja ya Olonda,11/1/1987, ptsa. 8-9
14 Atatero, anaitana gulu la anthuwo kuti abwerenso kwa iye ndipo anawauza kuti: “Mvetserani kuno nonsenu, ndipo mumvetse tanthauzo lake.+