Maliko 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atatero, anaitananso khamu la anthuwo kuti abwere kwa iye, ndipo anayamba kulankhula nawo kuti: “Mverani kuno nonsenu, ndipo mumvetse tanthauzo lake.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:14 Nsanja ya Olonda,11/1/1987, ptsa. 8-9
14 Atatero, anaitananso khamu la anthuwo kuti abwere kwa iye, ndipo anayamba kulankhula nawo kuti: “Mverani kuno nonsenu, ndipo mumvetse tanthauzo lake.+