-
Luka 3:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiyetu mubale zipatso zosonyeza kuti mwalapa. Ndipo musamadzinamize kuti, ‘Tili ndi atate wathu Abulahamu.’ Chifukwa ndikukuuzani kuti Mulungu akhoza kupangira Abulahamu ana kuchokera kumiyala iyi.
-