Luka 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyetu mubale zipatso zosonyeza kuti mwalapa.+ Ndipo musayambe kunena kuti, ‘Tili ndi atate wathu Abulahamu.’ Pakuti ndikukuuzani kuti Mulungu ali ndi mphamvu yokhoza kuutsira Abulahamu ana kuchokera ku miyala iyi.
8 Ndiyetu mubale zipatso zosonyeza kuti mwalapa.+ Ndipo musayambe kunena kuti, ‘Tili ndi atate wathu Abulahamu.’ Pakuti ndikukuuzani kuti Mulungu ali ndi mphamvu yokhoza kuutsira Abulahamu ana kuchokera ku miyala iyi.