Luka 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamene anali kunena mawu amenewa, mayi wina m’khamu la anthulo anafuula n’kumuuza kuti: “Ndi wodala mayi+ amene mimba yake inanyamula inu ndiponso amene munayamwa mabere ake!” Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:27 Yesu—Ndi Njira, tsa. 176 Nsanja ya Olonda,5/1/1989, tsa. 208/15/1988, tsa. 8
27 Pamene anali kunena mawu amenewa, mayi wina m’khamu la anthulo anafuula n’kumuuza kuti: “Ndi wodala mayi+ amene mimba yake inanyamula inu ndiponso amene munayamwa mabere ake!”