Luka 12:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 ndipo mukhale ngati anthu amene akuyembekezera kuti mbuye wawo abwere+ kuchokera ku ukwati,+ kuti akafika nʼkugogoda amutsegulire mwamsanga.
36 ndipo mukhale ngati anthu amene akuyembekezera kuti mbuye wawo abwere+ kuchokera ku ukwati,+ kuti akafika nʼkugogoda amutsegulire mwamsanga.