Luka 12:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Anthu achinyengo inu! Mumatha kuzindikira maonekedwe a dziko lapansi ndi kuthambo. Nanga zimakukanikani bwanji kuzindikira tanthauzo la zimene zikuchitika pa nthawi ino?+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:56 Nsanja ya Olonda,10/1/1988, tsa. 9
56 Anthu achinyengo inu! Mumatha kuzindikira maonekedwe a dziko lapansi ndi kuthambo. Nanga zimakukanikani bwanji kuzindikira tanthauzo la zimene zikuchitika pa nthawi ino?+