Luka 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 chifukwa amenewa ndi masiku opereka chiweruzo* kuti zonse zimene zinalembedwa zikwaniritsidwe.