Luka 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 chifukwa amenewa ndi masiku obwezera chilango, kuti zonse zimene zinalembedwa zikwaniritsidwe.+