Yohane 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye anali mʼdziko+ ndipo dziko linakhalapo kudzera mwa iye,+ koma dzikolo silinamudziwe. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:10 Nsanja ya Olonda,4/1/1993, tsa. 12