Yohane 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano anthu ambiri amene analipo pamene iye anaitana Lazaro kuti atuluke mʼmanda*+ nʼkumuukitsa, anapitiriza kumuchitira umboni.+
17 Tsopano anthu ambiri amene analipo pamene iye anaitana Lazaro kuti atuluke mʼmanda*+ nʼkumuukitsa, anapitiriza kumuchitira umboni.+