-
Yohane 12:48Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
48 Aliyense wondinyalanyaza komanso wosalandira mawu anga, ali naye mmodzi womuweruza. Mawu amene ine ndalankhula ndi amene adzamuweruze pa tsiku lomaliza.
-