Yohane 12:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Aliyense wondinyalanyaza ndi kusalandira mawu anga, ali naye mmodzi womuweruza. Mawu+ amene ine ndalankhula ndi amene adzamuweruze pa tsiku lomaliza. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:48 Nsanja ya Olonda,12/1/1989, tsa. 9
48 Aliyense wondinyalanyaza ndi kusalandira mawu anga, ali naye mmodzi womuweruza. Mawu+ amene ine ndalankhula ndi amene adzamuweruze pa tsiku lomaliza.