-
Machitidwe 2:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ndidzachita zodabwitsa kumwamba ndiponso zizindikiro padziko lapansi. Padzakhala magazi, moto ndi utsi wokwera mʼmwamba.
-