Machitidwe 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzachita zodabwitsa kuthambo ndi zizindikiro padziko lapansi. Ndidzachititsa kuti pakhale magazi, moto ndi mtambo wautsi.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:19 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, ptsa. 13-1412/15/1997, ptsa. 16-17
19 Ndidzachita zodabwitsa kuthambo ndi zizindikiro padziko lapansi. Ndidzachititsa kuti pakhale magazi, moto ndi mtambo wautsi.+