Machitidwe 2:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndipo ndi mawu enanso ambiri, Petulo anachitira umboni mokwanira. Komanso sanaleke kuwadandaulira kuti: “Dzipulumutseni ku mʼbadwo wa maganizo olakwikawu.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:40 Nsanja ya Olonda,6/1/1997, tsa. 28
40 Ndipo ndi mawu enanso ambiri, Petulo anachitira umboni mokwanira. Komanso sanaleke kuwadandaulira kuti: “Dzipulumutseni ku mʼbadwo wa maganizo olakwikawu.”+