Deuteronomo 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo ndi amene achita zinthu zoipa.+ Iwo si ana ake, ali ndi vuto ndi iwowo.+ Iwo ndi mʼbadwo wopotoka maganizo komanso wachinyengo!+ Salimo 78:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Akadzachita zimenezi sadzakhala ngati makolo awo,Mʼbadwo wosamva komanso wopanduka,+Mʼbadwo umene mtima wawo unali wosakhazikika*+Komanso wosakhulupirika kwa Mulungu.
5 Iwo ndi amene achita zinthu zoipa.+ Iwo si ana ake, ali ndi vuto ndi iwowo.+ Iwo ndi mʼbadwo wopotoka maganizo komanso wachinyengo!+
8 Akadzachita zimenezi sadzakhala ngati makolo awo,Mʼbadwo wosamva komanso wopanduka,+Mʼbadwo umene mtima wawo unali wosakhazikika*+Komanso wosakhulupirika kwa Mulungu.