Machitidwe 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma anthu ambiri amene anamvetsera mawu awo anakhulupirira, ndipo chiwerengero cha amuna chinakwana pafupifupi 5,000.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:4 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 35
4 Koma anthu ambiri amene anamvetsera mawu awo anakhulupirira, ndipo chiwerengero cha amuna chinakwana pafupifupi 5,000.+