Machitidwe 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Komanso, onse amene anakhulupirira anali ndi maganizo ofanana.* Panalibe aliyense amene ankanena kuti zinthu zimene anali nazo zinali zayekha. Zonse zimene anali nazo zinali za onse.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:32 Nsanja ya Olonda,12/1/1990, ptsa. 24-25
32 Komanso, onse amene anakhulupirira anali ndi maganizo ofanana.* Panalibe aliyense amene ankanena kuti zinthu zimene anali nazo zinali zayekha. Zonse zimene anali nazo zinali za onse.+