Machitidwe 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma Ayuda amene sanakhulupirire, anauza zoipa anthu a mitundu ina nʼkuwasokoneza maganizo kuti atsutsane ndi abalewo.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:2 Nsanja ya Olonda,12/1/1998, tsa. 16
2 Koma Ayuda amene sanakhulupirire, anauza zoipa anthu a mitundu ina nʼkuwasokoneza maganizo kuti atsutsane ndi abalewo.+