Machitidwe 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma pamene ophunzira anamuzungulira, anadzuka nʼkukalowa mumzinda. Tsiku lotsatira iye pamodzi ndi Baranaba anachoka nʼkupita ku Debe.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:20 Nsanja ya Olonda,2/15/2013, ptsa. 28-29
20 Koma pamene ophunzira anamuzungulira, anadzuka nʼkukalowa mumzinda. Tsiku lotsatira iye pamodzi ndi Baranaba anachoka nʼkupita ku Debe.+