Machitidwe 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Paulo anatsika pansi, ndipo anafika pamene iye anali nʼkumukumbatira.+ Kenako ananena kuti: “Khalani chete, chifukwa ali moyo tsopano.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:10 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 165 Nsanja ya Olonda,7/15/2000, ptsa. 12-13
10 Koma Paulo anatsika pansi, ndipo anafika pamene iye anali nʼkumukumbatira.+ Kenako ananena kuti: “Khalani chete, chifukwa ali moyo tsopano.”+