Machitidwe 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Paulo anaganiza zongolambalala Efeso,+ kuti asataye nthawi mʼchigawo cha Asia. Anachita zimenezi chifukwa ankafulumira kuti ngati nʼkotheka, pa tsiku la Chikondwerero cha Pentekosite akakhale ali ku Yerusalemu.+
16 Paulo anaganiza zongolambalala Efeso,+ kuti asataye nthawi mʼchigawo cha Asia. Anachita zimenezi chifukwa ankafulumira kuti ngati nʼkotheka, pa tsiku la Chikondwerero cha Pentekosite akakhale ali ku Yerusalemu.+