Aroma 3:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Popeza Mulungu ndi mmodzi,+ iye adzaona kuti anthu odulidwa ndi olungama+ chifukwa cha chikhulupiriro chawo. Adzaonanso kuti anthu osadulidwa ndi olungama+ chifukwa cha chikhulupiriro chawo.
30 Popeza Mulungu ndi mmodzi,+ iye adzaona kuti anthu odulidwa ndi olungama+ chifukwa cha chikhulupiriro chawo. Adzaonanso kuti anthu osadulidwa ndi olungama+ chifukwa cha chikhulupiriro chawo.