Aroma 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa tikudziwa kuti Chilamulo nʼchochokera kwa Mulungu kudzera mwa mzimu, koma ineyo si ine wangwiro ndipo ndinagulitsidwa ku uchimo.+
14 Chifukwa tikudziwa kuti Chilamulo nʼchochokera kwa Mulungu kudzera mwa mzimu, koma ineyo si ine wangwiro ndipo ndinagulitsidwa ku uchimo.+