Aroma 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mofanana ndi zimenezi, mzimu umatithandiza pa zimene tikulephera kuchita.+ Chifukwa vuto ndi lakuti sitidziwa zimene tikufunika kutchula popemphera, koma mzimu umachonderera mʼmalo mwathu ndi madandaulo amene sitinathe kuwafotokoza. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:26 Nsanja ya Olonda,11/15/2009, tsa. 76/1/2009, tsa. 306/15/2008, tsa. 304/15/2005, ptsa. 18-199/15/1992, ptsa. 16-1712/15/1991, tsa. 18
26 Mofanana ndi zimenezi, mzimu umatithandiza pa zimene tikulephera kuchita.+ Chifukwa vuto ndi lakuti sitidziwa zimene tikufunika kutchula popemphera, koma mzimu umachonderera mʼmalo mwathu ndi madandaulo amene sitinathe kuwafotokoza.
8:26 Nsanja ya Olonda,11/15/2009, tsa. 76/1/2009, tsa. 306/15/2008, tsa. 304/15/2005, ptsa. 18-199/15/1992, ptsa. 16-1712/15/1991, tsa. 18