Aroma 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno ndifunse kuti, kodi anapunthwa mpaka kugweratu? Ayi. Koma chifukwa cha kulakwa kwawo anthu a mitundu ina apeza chipulumutso, ndipo zimenezi zachititsa kuti olakwawo achite nsanje.+
11 Ndiyeno ndifunse kuti, kodi anapunthwa mpaka kugweratu? Ayi. Koma chifukwa cha kulakwa kwawo anthu a mitundu ina apeza chipulumutso, ndipo zimenezi zachititsa kuti olakwawo achite nsanje.+