Deuteronomo 32:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo andikwiyitsa* ndi milungu yabodza.+Andikhumudwitsa ndi mafano awo opanda pake.+ Choncho ine ndiwachititsa nsanje ndi anthu opanda pake,+Ndiwakhumudwitsa ndi mtundu wopusa.+ Aroma 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komanso ndifunse kuti, Kodi si zoona kuti Aisiraeli anadziwa?+ Choyamba Mose anati: “Ndidzakuchititsani nsanje pogwiritsa ntchito anthu omwe si Aisiraeli. Ndidzakukwiyitsani koopsa pogwiritsa ntchito mtundu wopusa.”+
21 Iwo andikwiyitsa* ndi milungu yabodza.+Andikhumudwitsa ndi mafano awo opanda pake.+ Choncho ine ndiwachititsa nsanje ndi anthu opanda pake,+Ndiwakhumudwitsa ndi mtundu wopusa.+
19 Komanso ndifunse kuti, Kodi si zoona kuti Aisiraeli anadziwa?+ Choyamba Mose anati: “Ndidzakuchititsani nsanje pogwiritsa ntchito anthu omwe si Aisiraeli. Ndidzakukwiyitsani koopsa pogwiritsa ntchito mtundu wopusa.”+