Aroma 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chitani zimenezi, makamakanso chifukwa chakuti nyengo ino mukuidziwa, kuti tili kale mu nthawi yoti mudzuke ku tulo,+ chifukwa panopa chipulumutso chathu chili pafupi kwambiri kusiyana ndi nthawi imene tinakhala okhulupirira. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:11 Nsanja ya Olonda,11/15/2013, tsa. 73/15/2012, tsa. 115/1/1992, tsa. 2310/1/1989, ptsa. 30-31
11 Chitani zimenezi, makamakanso chifukwa chakuti nyengo ino mukuidziwa, kuti tili kale mu nthawi yoti mudzuke ku tulo,+ chifukwa panopa chipulumutso chathu chili pafupi kwambiri kusiyana ndi nthawi imene tinakhala okhulupirira.