1 Akorinto 15:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Chifukwa matupi oti akhoza kuwonongekawa adzasintha nʼkukhala oti sangawonongeke.+ Ndipo matupi oti angafewa adzasintha nʼkukhala oti sangafe.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:53 Nsanja ya Olonda,2/15/2009, tsa. 257/1/1998, tsa. 20
53 Chifukwa matupi oti akhoza kuwonongekawa adzasintha nʼkukhala oti sangawonongeke.+ Ndipo matupi oti angafewa adzasintha nʼkukhala oti sangafe.+