2 Akorinto 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo, mtumwi wa Khristu Yesu mwa kufuna kwa Mulungu, limodzi ndi Timoteyo+ mʼbale wathu, ndikulembera mpingo wa Mulungu wa ku Korinto komanso oyera onse amene ali ku Akaya konse:+
1 Ine Paulo, mtumwi wa Khristu Yesu mwa kufuna kwa Mulungu, limodzi ndi Timoteyo+ mʼbale wathu, ndikulembera mpingo wa Mulungu wa ku Korinto komanso oyera onse amene ali ku Akaya konse:+