Afilipi 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Komabe, ngakhale kuti ndikuthiridwa ngati nsembe yachakumwa,+ ndikuwonjezera pa nsembe+ zimene inu mukupereka komanso pa utumiki wopatulika umene* mukuchita mokhulupirika. Choncho ndikusangalala ndipo nonsenu ndikukondwera nanu limodzi. Afilipi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2142 Nsanja ya Olonda,11/15/2000, tsa. 12
17 Komabe, ngakhale kuti ndikuthiridwa ngati nsembe yachakumwa,+ ndikuwonjezera pa nsembe+ zimene inu mukupereka komanso pa utumiki wopatulika umene* mukuchita mokhulupirika. Choncho ndikusangalala ndipo nonsenu ndikukondwera nanu limodzi.