6 umene unafika kwa inu. Uthenga wabwino ukubala zipatso ndiponso kufalikira padziko lonse.+ Zimenezi ndi zimenenso zakhala zikuchitika kwa inu kuyambira tsiku limene munamva ndi kudziwa molondola za kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu komwe ndi kwenikweni.