Akolose 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Uthenga wabwinowu unafika kwa inu popeza ukubala zipatso+ ndipo ukuwonjezeka+ m’dziko lonse.+ Ukuteronso pakati panu, kuyambira tsiku limene munamva ndi kudziwa molondola za kukoma mtima kwakukulu+ kwa Mulungu monga mmene kulilidi.+
6 Uthenga wabwinowu unafika kwa inu popeza ukubala zipatso+ ndipo ukuwonjezeka+ m’dziko lonse.+ Ukuteronso pakati panu, kuyambira tsiku limene munamva ndi kudziwa molondola za kukoma mtima kwakukulu+ kwa Mulungu monga mmene kulilidi.+