Akolose 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tikupemphanso kuti mulandire mphamvu zazikulu mogwirizana ndi mphamvu zake zochititsa mantha,+ nʼcholinga choti muthe kupirira zinthu zonse moleza mtima ndiponso mwachimwemwe, Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:11 Nsanja ya Olonda,11/1/2001, tsa. 185/15/1991, tsa. 20
11 Tikupemphanso kuti mulandire mphamvu zazikulu mogwirizana ndi mphamvu zake zochititsa mantha,+ nʼcholinga choti muthe kupirira zinthu zonse moleza mtima ndiponso mwachimwemwe,