Chivumbulutso 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mngelo woyamba ankaoneka ngati mkango.+ Mngelo wachiwiri ankaoneka ngati mwana wa ngʼombe wamphongo.+ Mngelo wachitatu+ anali ndi nkhope yooneka ngati ya munthu ndipo mngelo wa 4+ ankaoneka ngati chiwombankhanga chimene chikuuluka.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:7 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 80-81
7 Mngelo woyamba ankaoneka ngati mkango.+ Mngelo wachiwiri ankaoneka ngati mwana wa ngʼombe wamphongo.+ Mngelo wachitatu+ anali ndi nkhope yooneka ngati ya munthu ndipo mngelo wa 4+ ankaoneka ngati chiwombankhanga chimene chikuuluka.+