Chivumbulutso 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mngelo wachiwiri analiza lipenga lake. Ndipo chinachake chokhala ngati phiri lalikulu limene likuyaka moto chinaponyedwa mʼnyanja.+ Zitatero gawo limodzi mwa magawo atatu a nyanja, linasanduka magazi.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:8 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 134-136 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, tsa. 12
8 Mngelo wachiwiri analiza lipenga lake. Ndipo chinachake chokhala ngati phiri lalikulu limene likuyaka moto chinaponyedwa mʼnyanja.+ Zitatero gawo limodzi mwa magawo atatu a nyanja, linasanduka magazi.+