Chivumbulutso 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo gawo limodzi mwa magawo atatu a zamoyo zamʼnyanja zinafa.+ Komanso gawo limodzi mwa magawo atatu a ngalawa, linasweka. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:9 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 134-136 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, tsa. 12
9 Ndipo gawo limodzi mwa magawo atatu a zamoyo zamʼnyanja zinafa.+ Komanso gawo limodzi mwa magawo atatu a ngalawa, linasweka.