-
Chivumbulutso 21:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Komanso zitseko za mageti 12 aja zinali ngale 12. Chitseko chilichonse chinapangidwa ndi ngale imodzi. Ndipo msewu waukulu wamumzindawo unapangidwa ndi golide woyenga bwino woonekera ngati galasi.
-