Chivumbulutso 21:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma chilichonse chodetsedwa komanso aliyense wochita zonyansa ndiponso zachinyengo, sadzalowa mumzindawo.+ Amene adzalowemo ndi okhawo amene mayina awo analembedwa mumpukutu wa moyo wa Mwanawankhosa.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:27 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 306, 310
27 Koma chilichonse chodetsedwa komanso aliyense wochita zonyansa ndiponso zachinyengo, sadzalowa mumzindawo.+ Amene adzalowemo ndi okhawo amene mayina awo analembedwa mumpukutu wa moyo wa Mwanawankhosa.+