Genesis 39:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma Yehova anapitirizabe kukhala ndi Yosefe ndi kumusonyeza kukoma mtima kosatha. Ndipo anachititsa mkulu wa ndende kum’konda Yosefe.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 39:21 Nsanja ya Olonda,2/1/2015, tsa. 1211/1/2014, tsa. 155/15/2002, ptsa. 14-17
21 Koma Yehova anapitirizabe kukhala ndi Yosefe ndi kumusonyeza kukoma mtima kosatha. Ndipo anachititsa mkulu wa ndende kum’konda Yosefe.+