Genesis 45:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Yosefe anauza abale akewo kuti: “Ndine Yosefe! Kodi bambo anga ali moyobe?” Koma abale akewo sanathe kumuyankha chifukwa anali atawasokoneza maganizo.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:3 Nsanja ya Olonda,1/1/1999, tsa. 30
3 Kenako Yosefe anauza abale akewo kuti: “Ndine Yosefe! Kodi bambo anga ali moyobe?” Koma abale akewo sanathe kumuyankha chifukwa anali atawasokoneza maganizo.+