Genesis 46:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano nawa mayina a ana a Isiraeli, kapena kuti ana a Yakobo, omwe anabwera nawo ku Iguputo:+ Mwana woyamba wa Yakobo anali Rubeni.+
8 Tsopano nawa mayina a ana a Isiraeli, kapena kuti ana a Yakobo, omwe anabwera nawo ku Iguputo:+ Mwana woyamba wa Yakobo anali Rubeni.+