Genesis 46:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Amenewa ndiwo anali ana a Leya,+ amene anaberekera Yakobo ku Padana-ramu, kuphatikizapo Dina+ mwana wamkazi wa Yakobo. Ana ake onse aamuna ndi aakazi ndi adzukulu ake analipo 33.
15 Amenewa ndiwo anali ana a Leya,+ amene anaberekera Yakobo ku Padana-ramu, kuphatikizapo Dina+ mwana wamkazi wa Yakobo. Ana ake onse aamuna ndi aakazi ndi adzukulu ake analipo 33.