Genesis 46:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yosefe anabereka Manase+ ndi Efuraimu*+ ku Iguputo. Anabereka anawa kwa mkazi wake Asenati+ mwana wa Potifera, yemwe anali wansembe wa mzinda wa Oni.
20 Yosefe anabereka Manase+ ndi Efuraimu*+ ku Iguputo. Anabereka anawa kwa mkazi wake Asenati+ mwana wa Potifera, yemwe anali wansembe wa mzinda wa Oni.