Genesis 46:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno Yosefe anauza abale ake ndi a m’nyumba ya bambo ake kuti: “Ndipite kwa Farao ndikam’dziwitse.+ Ndikanene kuti, ‘Abale anga ndi a m’nyumba ya bambo anga, amene anali m’dziko la Kanani, abwera kuno kwa ine.+
31 Ndiyeno Yosefe anauza abale ake ndi a m’nyumba ya bambo ake kuti: “Ndipite kwa Farao ndikam’dziwitse.+ Ndikanene kuti, ‘Abale anga ndi a m’nyumba ya bambo anga, amene anali m’dziko la Kanani, abwera kuno kwa ine.+